Evance Jimu Foundation for Development

Evance Jimu Foundation for Development Together, we build hope and empower lives.

Evance Jimu Foundation for Development is a non-profit organization committed to supporting vulnerable children, elderly care, and community development in Malawi.

“Today I celebrate another year of life, grace, and purpose. I thank God for His faithfulness and everyone who has been ...
08/03/2026

“Today I celebrate another year of life, grace, and purpose. I thank God for His faithfulness and everyone who has been part of my journey. The best is yet to come.”

07/03/2026

Sometimes life gets tough, koma osataya mtima. Every challenge you face today is preparing you for a better tomorrow.

You may feel tired, mwina zinthu sizikuyenda monga momwe munaganizira, but remember this — giving up is not an option.

God did not bring you this far kuti akusiye pakati pa njira. Keep pushing, keep praying, and keep believing.

Nthawi yanu idzafika. What looks impossible today ikhoza kukhala testimony yanu mawa.

So this weekend, limbitsani mtima, pumulani pang’ono, koma musasiye kulota zazikulu.
Your story is not finished yet.
— Evance Jimu

04/03/2026

koma khalaniko mamuna mmodzi iii😂😂😂

04/03/2026

Pali ndani apa

02/03/2026

Takulandirani ku mwezi watsopano. Tikuthokoza Mulungu chifukwa watipatsa moyo ndi mwayi wina woyambiranso.

Ngati mwezi wapitawo unali wovuta, musataye mtima. Mwezi uno ndi mwayi watsopano wokonza zolakwa, kulimbikira pa maloto athu, ndi kupitiriza kuyenda ndi chikhulupiriro.

Mulungu akhoza kusintha zinthu nthawi iliyonse. Choncho tiyeni tipitirize kugwira ntchito, kupemphera, ndi kukhulupirira kuti zabwino zikubwera.

Ndikufunirani aliyense mtendere, thanzi labwino, ndi madalitso ochuluka mu mwezi uno.

Mwezi watsopano, chiyambi chatsopano.
— Evance Jimu

28/02/2026

From inbox
please tikufunafuna Garage imene ingatiphunzisire mwana wa 16yrs kukonza galimoto within Lilongwe, kawale , 23 and Petroda please akapezeka akuuzeni mitengo tikumane mwanayo school yamukanika amakanako

alipo angatithandize? ndiyankhuleni 0992819041

2030 my vote again mkulukutamoyo 😘
28/02/2026

2030 my vote again mkulukutamoyo 😘

28/02/2026

ñapepe ma admin anali busy apapa bundle ija tipitilizeno tsano

tiyuza ma number aja mwaponya mamawa

28/02/2026

Hello ku Blantyre àkufuna maid koma oyendera ku Mkolokosa salary akuti 75,000 amene Ali serious andilankhule ndupaseni connection imenei 0992819041 please osandiimbira just wasap

28/02/2026

Only Airtel mpaka 9am

28/02/2026

Mwauka bwanji nonse?
Moyo umatipatsa mwayi watsopano tsiku lililonse. Ngakhale dzulo zinthu zinali zovuta, lero ndi tsiku lina latsopano loyambiranso. Musalole zovuta za dzulo kukuberani chiyembekezo cha lero.

Tipemphere:
Ambuye Mulungu, tikukuthokozani chifukwa cha mphatso ya tsiku latsopano. Mutitsogolere pa zonse zomwe tikachite lero. Dalitsani ntchito za manja athu, mutipatse nzeru pa zisankho zathu, ndipo mutiteteze ife ndi mabanja athu. Tsegulani zitseko za mwayi ndi madalitso pa moyo wathu lero. Dzazani mitima yathu ndi mtendere ndi chiyembekezo. Amen.
Kumbukirani: Tsiku lililonse ndi chiyambi chatsopano. Khalani olimba mtima ndipo musataye chiyembekezo.
– Evance Jimu

27/02/2026

Ambuye Mulungu,
Tikukupemphani kuti mudalitse aliyense amene akuwerenga uthengawu. Mupereke mtendere m'mitima yawo, mulimbikitse pamene ali ofooka, ndipo mutsegule njira pamene zinthu zikuwoneka zovuta. Muwadalitse ndi thanzi labwino, nzeru, ndi chitetezo tsiku ndi tsiku. Nyumba zawo zidzaze ndi chikondi, chisomo, ndi madalitso anu. Amen.

Address

Nomzan
Cape Town
7620

Opening Hours

Monday 08:00 - 16:00
Tuesday 08:00 - 16:00
Wednesday 08:00 - 16:00
Thursday 08:00 - 16:00
Friday 08:00 - 16:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Evance Jimu Foundation for Development posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share