Bridge - Household & Domestic Staff Training School

Directions

Bridge - Household & Domestic Staff  Training School
Training service provider promoting skills development in the informal sector. Skills For Everyone! EDUCATE ! EMPOWER! CHANGE!

Our mission is to empower low income earners through skills training and entrepreneurship knowledge resulting in dignified work and equal access to business opportunities.

Household / Maids training! Free online training for 15 people only.To qualify; willing to learn must have access to Wha...
26/08/2026

Household / Maids training!
Free online training for 15 people only.
To qualify;
willing to learn
must have access to Whatsapp phone
must have national ID
Apply by sending your full name, age, s*x , location and 2 references.

WHY SHOULD YOU REGISTER? OR GET YOUR MAID TRAINED?SHORT COURSE!!!CHOLINGA CHA MA COURSE ATHU✔ Kupatsa anthu ogwira ntchi...
20/07/2026

WHY SHOULD YOU REGISTER? OR GET YOUR MAID TRAINED?

SHORT COURSE!!!

CHOLINGA CHA MA COURSE ATHU

✔ Kupatsa anthu ogwira ntchito zam’nyumba maphunziro ndi luso (skills) kuti athe kugwila ntchito mozindikila komanso mwaukadaulo.

✔ Kuwathandiza kukhala ndi mphamvu yokambirana (negotiate) malipiro abwino malingana ndi luso lawo

✔ Kuwatsegulira mwayi wogwira ntchito m’makomo ndi malo apamwamba

1. Maids training/ housekeeping course and other courses targeted at low income earners.

PHINDU

** Malipilo okwela, mwayi opeza high profile ntchito, lodges, diplomats and hotels.

✔ Certificate
✔ CV yolembedwa mwaluso
✔ Coaching ya interview ndi work tips
✔ Mwayo olandira malipiro abwino

Registration is Mk10,000
Fees
Mk75 000 - Week
Mk15 000 - per Day

We also have online lessons if you are outside Lilongwe
Online lessons is Mk50 000

Tili ku Area 49. Lilongwe

Call/ wap 0991 95 02 47

2026 REGISTRATIONILIMKATI!!!,Kuzani mwayi wanu  wantchito ndi malipilo okwela ndi Mamphunziro amenewa. Registration is M...
17/07/2026

2026 REGISTRATIONILIMKATI!!!,

Kuzani mwayi wanu wantchito ndi malipilo okwela ndi Mamphunziro amenewa.

Registration is Mk10,000
Fees Mk75 000

Nthawi : 1 week

We also have online lessons if you are outside Lilongwe
Online lessons is Mk50 000

Tili ku Area 49 . Lilongwe

Call/ Watsaap/text 0991950247
https://chat.whatsapp.com/GUqLmaBkoyTKo7fgVlAvxk

Maids training 2026 REGISTRATION ILIMKATI!!!, SHORT COURSE!!!Kuzani mwayi wanu  wantchito ndi malipilo okwela ndi Mamphu...
17/07/2026

Maids training

2026 REGISTRATION ILIMKATI!!!, SHORT COURSE!!!

Kuzani mwayi wanu wantchito ndi malipilo okwela ndi Mamphunziro amenewa.

Registration is Mk15,000
Fees Mk75 000

Nthawi : 1 week,

We also have online lessons if you are outside Lilongwe
Online lessons is Mk50 000

Tili ku Area 49. Lilongwe

Call/ Watsaap/text 0991950247
https://chat.whatsapp.com/GUqLmaBkoyTKo7fgVlAvxk

27/01/2026

Bridge Skills Hub - Skills For All

Educate/Empower/Change

WHO ARE WE?

We are a training service provider promoting skills development in the informal sector.
Our mission is to empower low income earners through skills training and entrepreneurship knowledge, resulting in dignified work and equal access to business opportunities.

WHY SHOULD YOU REGISTER?

CHOLINGA CHA MA COURSE ATHU

✔ Kupatsa anthu ogwira ntchito zam’nyumba maphunziro ndi luso (skills)

✔ Kuwathandiza kukhala ndi mphamvu yokambirana (negotiate) malipiro abwino

✔ Kuwatsegulira mwayi wogwira ntchito m’makomo ndi malo apamwamba

1. Maids training/ housekeeping course and other courses targeted at low income earners.

PHINDU

** Malipilo okwela, mwayi opeza high profile ntchito, lodges, diplomats and hotels.

✔ Certificate
✔ CV yolembedwa mwaluso
✔ Coaching ya interview ndi work tips
✔ Luso lolandira malipiro abwino

📚 MAPHUNZIRO / LESSONS

• Home / Household Management – Kuyendetsa Ntchito Zam’nyumba

• Home Safety & Security – Chitetezo ndi Kupewa Zovulaza M’nyumba

• Good Work Ethics & Communication – Makhalidwe Abwino Pantchito & Kulankhulana

• Work Etiquette & Manners – Makhalidwe Abwino Pantchito ndi Chikhalidwe

• Time Management – Kukonza Nthawi

• Conflict Resolution – Kuthetsa Zovuta / Mabvuto

• Psychosocial Counseling – Malangizo a M’maganizo ndi Chikhalidwe

REGISTRATION IN PROGRESS!!! LIMITED SPACE!!

Kuzani mwayi wanu wantchito, luso ndi malipiro abwino

LEMBETSANI LERO!! MALO ASANATHE

📝 Registration ili mkati

**No any qualification - chidwi ndi khama basi
** koma mukhale ndi cha unzika
**Mamphunziro alipo muchichewa ndi chizungu.

Maphunziro ayamba pa: 2 February 2026

SCHOOL FEES : MWK 150 000
ONLINE FEES: MWK 50 000

REGISTRATION FEES : MWK 10 000

PERIOD

MASABATA ( 4 - 6 Weeks )
Course takes 20- 30 days to complete
Minimum of 45 to 60 maximum credit hours

TIME TABLE

***PHYSICAL CLASSES

Monday - Friday :
9AM - 11AM / 1PM- 3PM

Saturday:
9AM - 11AM / 1PM - 3PM

Sundays : 1PM - 3PM

***ONLINE CLASSES ( watsaap)

weekdays: 7PM - 9 PM

Saturdays : 7PM - 9PM

LOCATION.
Area 49, Gulliver, Lilongwe
Calls/ Watsaap 0991950 247/ 0883142921

For registration and school fees , use the account below and send us proof of payment.

Bridge Skills Hub
First Capital Bank
0037502004197
Gateway Mall

✨ Invest in yourself kapena m’bale / mlongo wanu — mphatso yabwino kwambiri mu 2026 and forever!

2026 REGISTRATIONILIMKATI!!!,Kuzani mwayi wanu  wantchito ndi malipilo okwela ndi Mamphunziro amenewa. Registration is M...
21/01/2026

2026 REGISTRATIONILIMKATI!!!,

Kuzani mwayi wanu wantchito ndi malipilo okwela ndi Mamphunziro amenewa.

Registration is Mk10,000
Fees Mk150 000

Nthawi : 4 - 6 weeks

We also have online lessons if you are outside Lilongwe
Online lessons is Mk50 000

Tili ku Area 49,gulliver . Lilongwe

Call/ Watsaap/text 0991950247
https://chat.whatsapp.com/GUqLmaBkoyTKo7fgVlAvxk

Address

Area 25, Sector 5. Near Dzenza Sec School. Lioongwe.
Lilongwe
0000

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bridge - Household & Domestic Staff Training School posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share